Visit this profile later to see if your question was answered.
pang'ono
eti kuluza ndi ka team ka EUROPA eti? Zinandiwawa bwanji
ayi, zimenezo akunena ndi a Man Utd, cholinga chakuti tifanane ndi iwowo!!
eeeh iwe umafuna nditsalire?
kamwendo (Tili pano club) umati bwa?
mmmmmh! Maur?
nyoooooo!!!!
Deus ndi mlamu wanga,ndinagwira sistez yake ETTA
ligid, mbuli, sasamba
Ireen John.......bwa?
ine zotukwana ayi!!!
hehe! Abombination, munthune za akazi sindipanga!! Bt hey, let mi ask u, each question u ask is concerning *ex.....chifukwa?
inenso sindichidziwa
mmmmh! I'v neva, ndimaopa kuti angandionere!!
1 & half
hehehehe!!! Mafunso mbwerekete, ukufuna chithe? Ine sinditchula
eish koma iwe nde utikwanadi
1 & half.....umati bwa?
bush *ex.....muhahahahahaha!
hahahahahaha!! Maureen Mtambo Nsinja & Diana Chiutsi. Ngakhale ziri zitsiru
eeh! Chikodi Thandikily Chiutsi.....bwa?
kikikiki ndiri kuno aise!!! Owe_owe_owe!!
mxiiii!!! Opusa iwe eti
pa den,kudya nsima yanyemba
wamva kuti? Kafunsaneni komweko!!!
yes, that's true
kwatsala medical
ndinaledzera, bwa?
ndinawagulira ndine,moti leronso Chembe wamwa Fanta chifukwa chaine
izo ndizabodza, ine ndine mfana ofewa.....ndakhala ndi zibwenzi zambiri,achina Etta, Eliza jst to mention few
m'makanika kumufunsira inu
zopusa, ine nde ndidziyankha kuti chani? Mxiii
amayi anga ndi sistez ya nkoz!! Iwe ukuona bwa?
iwe mbuzi eti!!! Mafunso ngati kukhothi bwanji? Mxii
chomwe timakana nchakuti: Domina ndimunthu owoneka bwino kwambiri, choncho sangagwidwe ndi Gallas
ayi, sindikhala ndi anzanga otukwana! Munthu ameneyu amandionera kuipa,choncho muzimupempherera kuti mulungu asamamupatse zofuna zake! Kikikiki
ulipo wambiri, m'mati bwa?
I'v already said that i'm nice. I've neva heard rumours abt mi which aren't true
eish! Iyi nde mirandu tsopano
interigent, hardworker & nice