85
Replies
kodi zomba mental ili pati? Ndiyende bwanji kuti ndikamuone wapenga chifukwa cha mafras yu?
ili pafupi ndi maximum prison
nde mwati joel chiponde yo ali ku mental?
inde kumenekosa ati he has been listed as condemed patient
kodi zoti joel chiponde wapenga ndi zoona?
eya man pano ali ku zomba
KUFUPIKA TAMUWONENI
iwe siwafupi komabe akazi amakukanika
Ugwire koma, azinzako maswazi onse adagwira wasala wekha
swazi wankulu iwe unagwira?
udasiya kusuta chamba??
sinasuteko
a short man is a boy afta all ha ha ha hah Yoweli
oooh
eti zoona kuti umakhutila mmbali monga chitila tonde?
joel hahaha nzeru zakutheradi eti
Modern day Zakeyu otolera misonkho mxi!
kodi ku MRA umasilirako eti?
eti mkazi waku medicine adakusiyani chifukwa u r a short man? ha ha ha haha
nop...hu told u that lie?
kodi ugwira liti?
nthawi ikakwana, and yatsala pang'ono. Y asking?
a short man is not a boy ndaziwira pa iwe ha ha haha
mxi
man Paweni akuti maso ngati nandolo ha ha ha ha
lol maso a paweni ngati nandolo
eti every organ on ur body is short as well ha ah ha ha ha hah a hah just asking
kuganiza mopotoka ndichikwa akazi amakukanika
I really used to like u, i thought u werent one of those guys but now ndamva nyatsi zako
wamva chani joel?
IWE NDIWE MBUZI NDITHU, KUKANIKA KOPOSA, KUPEPERA, KUFUPIKA = IWE UKHALA K4 BASI HA HAAH A HA HAHA Yoweli
ndapepera cos ndakuuza kuti usiye kufuna azibale ako. Joel a.k.a Yokoniya u r a disgrace
I had a clash onu ku CHANCO
rily? Tiuzeni zambiri coz i dnt kno abt that
do u know who i am? guess...
yes a stupid fool 4rm soche
eti kufupika ngati chithumwa, mxi!...adakutembelera iwe, kubunyula too much
joel koma ugwire upeze chochita. Uleledzera kutukwana?
nkhanga ha ha haha
ndiwe opepela tonde iwe
Kodi Yoweli umalimbana naye ninji, chifukwa choti ndi mfana ofewa? machick amamufilatu heve
muhahaha dnt make me laugh, yoweli ofewa? He z jst a bunch of frustrated nerves
Basi busy kukhobola afana ofewa, kupepera basi
mxi nakukhobola kuti joel?opepera ndiwe u jst assume
Mumafuna mutagwira kma mumakanika, kupepera
imeneyo exprience yako joel eti
Kodi ka chick kaku MRA mumavaila kaja mudaponda?
anakuuzayo anakunamiza
kodi maso otongokao umauza ma babie kuti thats ur *exy appeal?
kodi ukumasowa zochita eti
mbuzi mwana mxi! Ugwre kma
ukundipangira zochita ngati ndani?
Ndiwe opepela heve
opepela ndiwe ayse
ka dzira la nkhanga, mxi!
mxi
Eti akazi amakukanani chifukwa cha kufupika kwanuko chifukwa hug yemwe amachita kugwada ha ha ha
its news 2 me
U r full of crap nkawona akazi amakukana dzira la nkhanga mxi!
my crap z none of yo busines. Learn 2 mind u own hater
Anthu afupinu mumandinyasa heve!
osalenga dziko lako ndikuikamo anthu atali okhaokha bwa? Mxi
Kodi umakanika kugwira chifukwa chani?
atate uswazi sikufunatu oho
Ine ndimakufuna kungoti iweyo kulimba 2 much, mxi! ndinasiya kukufila
mxi hu r u?
Eti ndi zoona kuti muli mwana, asikana ankakuseweresani maliseche??
ayi ilo ndi bodza
anakulora ndi angati?
u dnt wanna kno coz...
unafumsirapo akazi angati?
7 only and u?
eti umahopela mbale wako? ha ha ha
ayi dont confuse me wit joel
munayamba mwadyako ka nyama koboila? ha ha ha ha
if u mean nyama as 'nyama' then yes
munasiya ma wet dreams? ha ha ha ha
hahaha sizimasiyika zimenezija amwene mwina kwa anthu okwatirawo lol
Komano simumanzimvera chisoni kuti simunayambe mwakondapo??
anakunamiza ndani kuti sindinachiteko bwino
Inutu ndinu opepera kwambiri
chabwino inu ndi adolo
Koma inuyo 4-0 ndithu with zero attempts, kukhwima chani??
hahaha ndipo sindilipo ndekha kuli unyinji wit thc record
inuyo mukaziwona, monga simumnazimvera chisoni kuti palibe mkazi amene adayamba wakufunanipo??
sanandifuneko? Wats yo source? Citation needed
Kodi 4-0 imeneyi mukayiganizira, siimakuwawani??
hahaha iwe watumidwa ndi ndani kuti undifuse
kodi munachoka ndi 4-0 chifukwa chani?
tactically i was outclassed lol
eti simunayambe mwauzidwapo mau oti i luv u mmoyo mwanu monse??
hu told u that lie. Iwedi uli ngati ntaba eti
eti ndi zoona kuti even mahule amakukanani?? ha aha ha
mahule sangalore munthu wa smart ngati ine. Koma iweyo
kodi ndi zoona kuti munaponda kwa Bridget?
ayi ameneyo ndi joel
Eti ndi zoona zoti mpaka abusa aMazizwa adafika pokumphelerani kuti mugwire, after 4-0 yanu itawamvesa chisoni?? ha ha ha ha
hahaha its news 2 me
Kodi Joel Chiponde ukulimbana naye kwambiriyu, ndi Idol wako eti?....
ayi ndi kape winawake amandisake...mwana osasamba ngati uyo.
Eti mumapikisana ndi Henry Moyo in terms of uswazi?
ayi ndimapikisana ndi iweyo
Eti munkumutuma Kumbu kuti akufunsilireni mayearo?...
ayi zimenezo akufalitsa ndi mdani wanga Joel Chiponde ndi amithenga ake
Inu ndi opepera inu, nkawona simutha kufunsira ha ha ha.....
iweyo unafusirako? Kape
upite ku ubusa chabwino, wachita uchimo wambiri pakuganiza than pakuchita komwe Zakeyu wotolera misonkho iwe ha ha ha
chabwino iwe sumachimwa
Zakeyu otolera misonkho ha ha ha ah
komatu kuli kwacha
upite kui umsembe iwe apa mxi!
unfortunately am not a catholic
Kodi umazitenga ngati ndani iwe??...
munthu ofunikira ndi waphindu kuposa iweyo
eti munali chairman wamafumu aparrellel alongside Twambi?? ha ha ha ha
not me mwina twambi yo
eti mukadali virigo???
limeneli lokha sindiyankha
Inu monga otolela msonkho, zoona ndalama zonse zija ku MRAko olo despa osagwira olo???
ngati mukuzifuna za msonkho osangopempha bwa
eti ndi zoona ma graduates anzanu amakukanani th@z why mumagwira maperi okhaokha???
chabwino iweyo joel uli ndi chibwezi graduate
uswazi kuchita kumatilira ngati litsiro, do something abt it man
kodi iwe umadzitenga ofewa?
eti munalandidwapo mkazi ndi yearo??
hahaha unakunamiza ndani?
Kulimba ngati kachigulumwa
chabwino inu ndiofewa
sopano mwapeza despano wapa COM? derby idakukanikani?
hahaha choka iwe chimunthu chosamva...kumamvetsetsa
is it true pa CHANCO munachokapo ndi 4-0 with zero attempts at goal?
hahaha koma ndigwirakobe pa c.o.m nyo
mukamaziona, do u think its possible muzagwirapo?
iwe ukukaika?
Eti uswazi wanu umaposa wa Alfred Mkaka?
hahaha nde wanditayatu
Kufupika ngati manganya
hahaha u co thc real qn?
iwe ndiwe opepera heve..u r not man enough 2 answer real questions
hahaha dikira ndiyankhe
ndiwe ogwira
fuso limeneli undifusa kangati?
eti umapanga umavu pa kumbu?
joel, eti unakanika kutchula kwa kumbu?
wat r u doing?
watching futbo
Still searching..lyk r u rily rily serious.....
do i sound joking? Nwe hu r u
Eti umafanana ndi Dzira la nkhanga? Kwex
is thc paweni or joel? Mxi
ndiwe wogwira???
no am searching..y asking?
ha ha ha ndi iwe eti? Ndakuziwa Yoweli
iwe ndi opepela eti u mean mwayi kachapila sumamudziwa?
iwe ndi opepela iwe
joel ulandire yesu
ukumafunsa mafunso opusa, anthu akuziwa uyaluka uwonanso Yoweli
mxi usandinamizire uli iwe ndi brian
Jus hrd news about ur girl that sh z datng a lot of men ukuchitapo chani????
which gal, u mean my ex?
Describe yourself in 3 words?
hahaha dnt kno maself
What's the one rumour you've heard about you that is not true?
mwatumidwa eti?
Who are you dating currently
y do u want 2 kno
VIEW MORE